Saturday, March 12, 2011

NDONDOMEKO YA MAPHUNZIRO NDI ZOCHITIKA PA MIBINDIKIRO YA CATHOLIC CHARISMATIC RENEWAL MOVEMENT KU NAMULENGA PARISH

with Richard Chirombo
1. Kuchita kafukufuku ndi kuunikira mobweleza bweleza ma membala ndi cholinga choti athe kuchotsa machinga a uzimu ndi kuzama mu Chikristu.


2. Mitu ya maphunziro

i. Za chikondi cha Mulungu Atate pa ine. (God the Father loves you personally)

ii. Ambuye Yesu anabwera kudzatipulumutsa ndi kutiombola ku ukapolo wa Satana, machimo ndi imfa. (Jesus saves you and sets you free)

iii. Yesu ndi Mbuye ndi Mpulumutsi wa moyo wanga (Jesus is Lord of my life.)

iv. Taitanidwa kukhala ophunzira a Yesu Kristu, tisenze Ntanda timulondole. (You are called to be a disciple of Jesus)

v. Ambuye Yesu anatitumizira Mzimu Woyera. (Jesus sends us his Holy Spirit)

vi. Mudzalandira Mzimu Woyera ndi mphatso zake (you will receive power from the Holy Spirit)

vii. Ndinu thupi la Khristu (You are the body of Christ)

viii. Mudzakhala mboni zanga (you shall be my witnesses)

No comments: