Tuesday, July 20, 2010

Ntasa Times' comments on lies that some chiefs are against Bingu's allocation of land for university construction

Posted with permission from Thom Chiumia:

Chambulamasokumutukowachambulamutukumasokowa says:
July 20, 2010 at 5:53 am
Dziko lino anthu okanika kwambiri ndi aphungu chifukwa ambiri ali ndi mantha kwambiri! Akuipopa kwambiri Ngwazi palibe amene amaiudza za nzero! Onse basi amafuna kuti akhulupirike koma chonsecho mukuononga dziko la Malawi! Kodi zokamanga ku farm ya munthu zadza ndi ndani! Bwanji osafuna malo ena opanda bvuto lilonse! Dziko lapita ku pompho ili!

Reply to this Comment
ntafu says:
July 20, 2010 at 6:25 am
Koma nkhani iyi ndiye mbolanso. Full of contradictions. if at all it is true all that has been written in this article, am not surprised because those chiefs are illiterate. so they don’t see the benefit of having a university in their locality. Koma abale kutsaphunzira ndi matendanso ena apadera.

Reply to this Comment
akumudzi says:
July 20, 2010 at 7:21 am
the title and the story does not tarry .Good title would have been that one you are thinking of university not apriority chiefs

Reply to this Comment
bikiloni difikoti says:
July 20, 2010 at 7:49 am
manje awa a president saziwa kuti wana wa univesite akakwiya amakhala violent. Sono nyumba yake iyo izakhala target. Iwo a president azakwanitsa kuthamanga ni kwendo yotchoka. Wasiyeni awo malo azawalira weka

Reply to this Comment
Navingod'o says:
July 20, 2010 at 8:33 am
Mafumu opusa inu kwabasi, you think its wealthy to cultivate that land than to construct a University??? Mlomwe ndi Mlomwe basi alibe ulemu/kuthokoza. M’malo moti muzinyadila kuti mukhala ndi University pafupi koma now u r complaining ndi nkhani zanu zopusazo.

Reply to this Comment
wakukaya says:
July 20, 2010 at 11:56 am
This is WALOMWE prezident sono muthana notha we see nothing here in the north so ur varsity kumakanganso .Today chilichonse ndi MTL M=Mulanje,T=Thyolo, Limited,any development start from there eve pa TV news is MTL sono vinu ivo

Reply to this Comment
kasaukani says:
July 20, 2010 at 11:58 am
bravo Bingu. These Thyolo people they don’t deserve that land for cultivation. Don’t give them room for we can loose the cheap labour in our fodya estates in the central region.

Reply to this Comment
Kazitape says:
July 20, 2010 at 12:10 pm
Why not upgrade the then Amalika Training Base to a University, Mr. President, instead of using part of your Ndata Farm???

Reply to this Comment
mpumulo ndatopa says:
July 20, 2010 at 12:13 pm
univesite osamanga ku blantyre bwanji? amalawi basi mukufuna muzizati univesite ndi yanu..mmene ankapangila ngwazi ndi KA?

Reply to this Comment
Masida says:
July 20, 2010 at 12:51 pm
I appreciet the idea of government constructing new universities. But I do not support the university being constructed in the vicinety of the president retirement resident. Lets watch out this, Why build a poly inside Sanjika or Chanco inside Zomba state house, for what. Yake kapena chani. Zibwana zachabechabe izi.

On the other hand, I also do not support what these chiefs are saying. There is a program called Kuzigulira malo, that targeted Mulanje and Thyolo for the good reasons the chief is saying, but thyolo was eventually removed as the people of Thyolo were selling the land government buys for them and going back to their old squashed up places.

Obviously government will not buy the chiefs talkes but also klet them find another location for the University, not Ndata.

No comments: