Friday, March 5, 2010

Bingu wa Mutharika's government is failing Malawians on passport fee

Look at the passport fee; chamba eti? Ndalama zake zichokera kuDPP kodi?
Inu mukudya mabwinobwino ndivimaallowance koma mukufuna mlimi wakuMalawi ngati Orchestra Kamanga ndianzake alipire Passport moduma akagulitsa fodya wawo!?
Do you pay for your passports you, anthu adyera.

Koma DPP guys and guyesses!

Should we subsidise your failures you government Yes Bwanas? Nonsense. I will not pay the new fee.
Bola John Chilembwe yemwe uja!

No comments: